Numeri 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Azichotsa phulusa* paguwa lansembe+ nʼkuyalapo nsalu ya ubweya wa nkhosa wapepo.