Numeri 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Ndipo azichotsa phulusa losakanizika ndi mafuta la paguwa lansembe+ n’kuyalapo nsalu ya ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira.
13 “Ndipo azichotsa phulusa losakanizika ndi mafuta la paguwa lansembe+ n’kuyalapo nsalu ya ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira.