-
Numeri 4:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Aziikapo ziwiya zonse zimene amagwiritsa ntchito akamatumikira paguwa lansembe. Aziikapo zoikamo phulusa la zingwe za nyale, mafoloko aakulu, mafosholo, mbale zolowa ndi ziwiya zonse zapaguwa lansembe.+ Ndiyeno aziziphimba ndi zikopa za akatumbu, nʼkubwezeretsa mʼmalo mwake ndodo zake zonyamulira.+
-