Numeri 4:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Amenewa ndi anthu amene anawerengedwa kuchokera mʼmabanja a ana a Kohati, onse amene ankatumikira pachihema chokumanako. Mose ndi Aroni anawawerenga pomvera zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+
37 Amenewa ndi anthu amene anawerengedwa kuchokera mʼmabanja a ana a Kohati, onse amene ankatumikira pachihema chokumanako. Mose ndi Aroni anawawerenga pomvera zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+