Numeri 4:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Awa ndiwo anawerengedwa+ mwa mabanja a ana a Kohati, onse otumikira m’chihema chokumanako, amene Mose ndi Aroni anawawerenga pomvera mawu a Yehova kwa Mose.
37 Awa ndiwo anawerengedwa+ mwa mabanja a ana a Kohati, onse otumikira m’chihema chokumanako, amene Mose ndi Aroni anawawerenga pomvera mawu a Yehova kwa Mose.