Numeri 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthuyo aziulula+ tchimo limene wachita. Azipereka malipiro onse a mlandu wake, komanso aziwonjezerapo limodzi mwa magawo 5 a malipirowo.+ Azipereka malipirowo kwa munthu amene wamulakwira.
7 Munthuyo aziulula+ tchimo limene wachita. Azipereka malipiro onse a mlandu wake, komanso aziwonjezerapo limodzi mwa magawo 5 a malipirowo.+ Azipereka malipirowo kwa munthu amene wamulakwira.