Numeri 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 mwakuti mwamuna wina wagona naye,+ koma mwamuna wake sanadziwe komanso palibe aliyense amene wadziwa. Muzichita zimenezi ngati mkaziyo wadzidetsa, koma palibe munthu amene angachitire umboni za nkhaniyo komanso sanagwidwe:
13 mwakuti mwamuna wina wagona naye,+ koma mwamuna wake sanadziwe komanso palibe aliyense amene wadziwa. Muzichita zimenezi ngati mkaziyo wadzidetsa, koma palibe munthu amene angachitire umboni za nkhaniyo komanso sanagwidwe: