-
Numeri 5:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 kapena ngati mwamuna akuchita nsanje ndipo akuganiza kuti mkazi wake sanayende bwino. Zikatero, mwamunayo azibwera ndi mkazi wake pamaso pa Yehova, ndipo wansembe azichita zonse zofunika pa mkaziyo mogwirizana ndi lamulo limeneli.
-