-
Numeri 5:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 kapena pamene mwamuna wakhala ndi nsanje mumtima mwake, ndipo akuganiza kuti mkazi wake sanayende bwino. Zikatero, mwamunayo aziimiritsa mkazi wake pamaso pa Yehova, ndipo wansembe azichita zonse zofunika pa mkaziyo malinga ndi lamulo limeneli.
-