-
Numeri 15:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Izi nʼzimene mukuyenera kumakachita popereka ngʼombe yamphongo iliyonse, nkhosa yamphongo iliyonse, mwana wa nkhosa wamphongo aliyense kapena mbuzi iliyonse.
-