-
Numeri 15:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Izi n’zimene muyenera kuchita popereka ng’ombe yamphongo iliyonse, nkhosa yamphongo iliyonse, mwana wa nkhosa wamphongo, kapena mbuzi.
-