Numeri 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ngati mlendo amene akukhala nanu kapena amene wakhala nanu kwa mibadwomibadwo, akufuna kupereka nsembe yowotcha pamoto yakafungo kosangalatsa* kwa Yehova, azikachita ngati mmene inu mukuchitira.+
14 Ngati mlendo amene akukhala nanu kapena amene wakhala nanu kwa mibadwomibadwo, akufuna kupereka nsembe yowotcha pamoto yakafungo kosangalatsa* kwa Yehova, azikachita ngati mmene inu mukuchitira.+