Numeri 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Ngati mlendo wokhala pakati panu, kapena mlendo amene wakhala nanu kwa mibadwomibadwo, afunikira kupereka nsembe yotentha ndi moto yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova, monga mmene inuyo muzichitira, iyenso azichita momwemo.+
14 “‘Ngati mlendo wokhala pakati panu, kapena mlendo amene wakhala nanu kwa mibadwomibadwo, afunikira kupereka nsembe yotentha ndi moto yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova, monga mmene inuyo muzichitira, iyenso azichita momwemo.+