Numeri 15:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Lankhula ndi Aisiraeli ndipo uwauze kuti azisokerera ulusi mʼmphepete mwa zovala zawo, ku mibadwo yawo yonse. Azisokereranso chingwe cha buluu pamwamba pa ulusi wa mphepete mwa zovalazo.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:38 Nsanja ya Olonda,7/15/2011, tsa. 128/1/2004, tsa. 267/15/2003, tsa. 13
38 “Lankhula ndi Aisiraeli ndipo uwauze kuti azisokerera ulusi mʼmphepete mwa zovala zawo, ku mibadwo yawo yonse. Azisokereranso chingwe cha buluu pamwamba pa ulusi wa mphepete mwa zovalazo.+