Numeri 15:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, uwauze kuti azisokerera mphonje m’mphepete mwa zovala zawo, ku mibadwo yawo yonse. Azisokereranso chingwe cha buluu pamwamba pa mphonje za zovalazo.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:38 Nsanja ya Olonda,7/15/2011, tsa. 128/1/2004, tsa. 267/15/2003, tsa. 13
38 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, uwauze kuti azisokerera mphonje m’mphepete mwa zovala zawo, ku mibadwo yawo yonse. Azisokereranso chingwe cha buluu pamwamba pa mphonje za zovalazo.+