Numeri 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lankhula ndi Aisiraeli, ndipo utenge ndodo imodzi kuchokera ku fuko lililonse, kwa mtsogoleri wa fukolo.+ Zikhalepo ndodo 12 ndipo ulembe dzina la mtsogoleri aliyense pa ndodo yake.
2 “Lankhula ndi Aisiraeli, ndipo utenge ndodo imodzi kuchokera ku fuko lililonse, kwa mtsogoleri wa fukolo.+ Zikhalepo ndodo 12 ndipo ulembe dzina la mtsogoleri aliyense pa ndodo yake.