Numeri 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, ndipo utenge ndodo+ ya fuko lililonse kwa mtsogoleri+ wa fukolo. Zikhalepo ndodo 12. Pandodo iliyonse ulembepo dzina la mtsogoleri wa fukolo.
2 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, ndipo utenge ndodo+ ya fuko lililonse kwa mtsogoleri+ wa fukolo. Zikhalepo ndodo 12. Pandodo iliyonse ulembepo dzina la mtsogoleri wa fukolo.