-
Numeri 17:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kenako Mose anatenga ndodo zonse pamaso pa Yehova nʼkupita nazo kwa Aisiraeli onse. Atsogoleri aja anayangʼana ndodozo, ndipo aliyense anatengapo yake.
-