-
Numeri 17:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Tsopano Mose anachotsa ndodo zonse pamaso pa Yehova n’kupita nazo kwa ana a Isiraeli onse. Amuna aja anayang’ana ndodozo, ndipo aliyense anatengapo yake.
-