Numeri 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Inuyo ndi amʼnyumba mwanu muzidya zimenezo pamalo alionse, chifukwa amenewo ndi malipiro anu pa utumiki umene muzichita pachihema chokumanako.+
31 Inuyo ndi amʼnyumba mwanu muzidya zimenezo pamalo alionse, chifukwa amenewo ndi malipiro anu pa utumiki umene muzichita pachihema chokumanako.+