Numeri 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Inuyo ndi a m’nyumba zanu muzidya zimenezo pamalo alionse, chifukwa ndizo malipiro anu pa utumiki umene muzichita m’chihema chokumanako.+
31 Inuyo ndi a m’nyumba zanu muzidya zimenezo pamalo alionse, chifukwa ndizo malipiro anu pa utumiki umene muzichita m’chihema chokumanako.+