Numeri 18:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mukapereka zinthu zabwino koposa kuchokera pa zinthu zimenezi, simudzachimwa ngati mutadya, komanso musaipitse zinthu zopatulika za Aisiraeli, kuti musafe.’”+
32 Mukapereka zinthu zabwino koposa kuchokera pa zinthu zimenezi, simudzachimwa ngati mutadya, komanso musaipitse zinthu zopatulika za Aisiraeli, kuti musafe.’”+