Numeri 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mʼmwezi woyamba, gulu lonse la Aisiraeli linafika mʼchipululu cha Zini, ndipo anthuwo anakhala ku Kadesi.+ Kumeneko nʼkumene Miriamu+ anafera nʼkuikidwa mʼmanda.
20 Mʼmwezi woyamba, gulu lonse la Aisiraeli linafika mʼchipululu cha Zini, ndipo anthuwo anakhala ku Kadesi.+ Kumeneko nʼkumene Miriamu+ anafera nʼkuikidwa mʼmanda.