Numeri 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma anthuwo anasowa madzi pamalopo,+ ndipo anasonkhana nʼkuukira Mose ndi Aroni.