Numeri 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma anthuwo anasowa madzi pamalopo, ndipo khamu+ lonselo linasonkhana n’kuukira Mose ndi Aroni.+