Numeri 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Tenga ndodo ndipo iweyo ndi mʼbale wako Aroni, musonkhanitse gulu lonse la anthuwo. Muuze thanthwe pamaso pawo kuti litulutse madzi. Utulutse madzi mʼthanthweli kuti upatse gululo, kuti limwe limodzi ndi ziweto zawo.”+
8 “Tenga ndodo ndipo iweyo ndi mʼbale wako Aroni, musonkhanitse gulu lonse la anthuwo. Muuze thanthwe pamaso pawo kuti litulutse madzi. Utulutse madzi mʼthanthweli kuti upatse gululo, kuti limwe limodzi ndi ziweto zawo.”+