Numeri 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Mose ndi Aroni anasonkhanitsa mpingo wonse pamodzi patsogolo pa thanthwelo, ndipo Mose anawauza kuti: “Tsopano tamverani anthu opanduka inu! Kodi tikutulutsireni madzi mʼthanthweli?”+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:10 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2018, ptsa. 14-15 Nsanja ya Olonda,9/1/2009, tsa. 1910/15/1987, ptsa. 30-31
10 Kenako Mose ndi Aroni anasonkhanitsa mpingo wonse pamodzi patsogolo pa thanthwelo, ndipo Mose anawauza kuti: “Tsopano tamverani anthu opanduka inu! Kodi tikutulutsireni madzi mʼthanthweli?”+
20:10 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2018, ptsa. 14-15 Nsanja ya Olonda,9/1/2009, tsa. 1910/15/1987, ptsa. 30-31