Numeri 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Paja makolo athu anapita ku Iguputo+ ndipo tinakhala kumeneko zaka zambiri.*+ Aiguputowo ankatizunza ifeyo limodzi ndi makolo athu.+
15 Paja makolo athu anapita ku Iguputo+ ndipo tinakhala kumeneko zaka zambiri.*+ Aiguputowo ankatizunza ifeyo limodzi ndi makolo athu.+