Numeri 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Aisiraeliwo anayankha kuti: “Ife tidzangodutsa mumsewu waukulu, ndipo ngati ifeyo kapena ziweto zathu tingamwe madzi anu, tidzakulipirani.+ Sitikufuna chilichonse ayi, koma kungodutsa mʼdziko lanu basi.”+
19 Aisiraeliwo anayankha kuti: “Ife tidzangodutsa mumsewu waukulu, ndipo ngati ifeyo kapena ziweto zathu tingamwe madzi anu, tidzakulipirani.+ Sitikufuna chilichonse ayi, koma kungodutsa mʼdziko lanu basi.”+