Numeri 26:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ana aamuna a Eliyabu anali Nemueli, Datani ndi Abiramu. Awiriwa, Datani ndi Abiramu, ndi amene anasankhidwa pa gululo ndipo anagwirizana ndi gulu la Kora+ pokangana ndi Mose+ komanso Aroni pamene ankatsutsana ndi Yehova.+
9 Ana aamuna a Eliyabu anali Nemueli, Datani ndi Abiramu. Awiriwa, Datani ndi Abiramu, ndi amene anasankhidwa pa gululo ndipo anagwirizana ndi gulu la Kora+ pokangana ndi Mose+ komanso Aroni pamene ankatsutsana ndi Yehova.+