Numeri 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zitatero, nthaka inangʼambika* nʼkuwameza. Koma Kora anafa pamene moto unapsereza amuna 250.+ Ndipo iwo anakhala chitsanzo chotichenjeza.+
10 Zitatero, nthaka inangʼambika* nʼkuwameza. Koma Kora anafa pamene moto unapsereza amuna 250.+ Ndipo iwo anakhala chitsanzo chotichenjeza.+