Numeri 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana aamuna a Simiyoni+ potengera mabanja awo anali awa: Nemueli amene anali kholo la banja la Anemueli, Yamini amene anali kholo la banja la Ayamini, Yakini amene anali kholo la banja la Ayakini,
12 Ana aamuna a Simiyoni+ potengera mabanja awo anali awa: Nemueli amene anali kholo la banja la Anemueli, Yamini amene anali kholo la banja la Ayamini, Yakini amene anali kholo la banja la Ayakini,