Numeri 26:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ana aamuna a Aseri+ potengera mabanja awo anali awa: Imuna amene anali kholo la banja la Aimuna, Isivi amene anali kholo la banja la Aisivi ndi Beriya amene anali kholo la banja la Aberiya.
44 Ana aamuna a Aseri+ potengera mabanja awo anali awa: Imuna amene anali kholo la banja la Aimuna, Isivi amene anali kholo la banja la Aisivi ndi Beriya amene anali kholo la banja la Aberiya.