Numeri 26:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Koma Nadabu ndi Abihu anafa chifukwa chopereka moto wosaloleka pamaso pa Yehova.+