-
Numeri 29:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Popereka ngʼombe zamphongo, nkhosa zamphongo ndi ana a nkhosa amphongo, muziperekanso nsembe zake zambewu ndi nsembe zake zachakumwa, mogwirizana ndi kuchuluka kwa nyamazo, potsatira dongosolo la nthawi zonse.
-