Numeri 29:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Popereka nyama zimenezi, ng’ombe zamphongo, nkhosa zamphongo, ndi ana a nkhosa amphongo, muziperekanso nsembe zake zambewu+ ndi nsembe zake zachakumwa,+ malinga ndi kuchuluka kwa nyamazo, potsatira dongosolo la nthawi zonse.+
30 Popereka nyama zimenezi, ng’ombe zamphongo, nkhosa zamphongo, ndi ana a nkhosa amphongo, muziperekanso nsembe zake zambewu+ ndi nsembe zake zachakumwa,+ malinga ndi kuchuluka kwa nyamazo, potsatira dongosolo la nthawi zonse.+