Numeri 29:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pa tsiku la 7, muzipereka ngʼombe 7 zamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo ndi ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi, zonse zizikhala zopanda chilema.+
32 Pa tsiku la 7, muzipereka ngʼombe 7 zamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo ndi ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi, zonse zizikhala zopanda chilema.+