Numeri 29:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “‘Pa tsiku la 7, muzipereka ng’ombe 7 zamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo, ndi ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi, wopanda chilema.+
32 “‘Pa tsiku la 7, muzipereka ng’ombe 7 zamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo, ndi ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi, wopanda chilema.+