Numeri 30:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ngati mwamunayo wafafaniza malonjezowo patapita nthawi kuchokera pa tsiku limene anamva malonjezowo, mwamunayo ndi amene aziyankha mlandu mʼmalo mwa mkazi wakeyo.+
15 Koma ngati mwamunayo wafafaniza malonjezowo patapita nthawi kuchokera pa tsiku limene anamva malonjezowo, mwamunayo ndi amene aziyankha mlandu mʼmalo mwa mkazi wakeyo.+