Numeri 30:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo ngati mwamunayo afafaniza malonjezowo patapita nthawi pambuyo poti wawamva kale, cholakwa chizikhala pa iyeyo m’malo mwa mkazi wake.+
15 Ndipo ngati mwamunayo afafaniza malonjezowo patapita nthawi pambuyo poti wawamva kale, cholakwa chizikhala pa iyeyo m’malo mwa mkazi wake.+