Numeri 35:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ngati munthu wafa wina atamukankha chifukwa chodana naye, kapena ngati wafa wina atamugenda ndi chinachake ndi zolinga zoipa,*+
20 Ngati munthu wafa wina atamukankha chifukwa chodana naye, kapena ngati wafa wina atamugenda ndi chinachake ndi zolinga zoipa,*+