Numeri 35:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo ngati chifukwa chodana naye anamukankha,+ kapena ngati anamulasa ndi chinthu atamubisalira,+ mnzakeyo n’kufa,
20 Ndipo ngati chifukwa chodana naye anamukankha,+ kapena ngati anamulasa ndi chinthu atamubisalira,+ mnzakeyo n’kufa,