Numeri 36:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Atsogoleri a mabanja omwe anachokera mwa Giliyadi mwana wa Makiri,+ mwana wa Manase, ochokera kumabanja a ana a Yosefe, anapita kukalankhula ndi Mose komanso akalonga omwe anali atsogoleri a Aisiraeli.
36 Atsogoleri a mabanja omwe anachokera mwa Giliyadi mwana wa Makiri,+ mwana wa Manase, ochokera kumabanja a ana a Yosefe, anapita kukalankhula ndi Mose komanso akalonga omwe anali atsogoleri a Aisiraeli.