Numeri 36:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Atsogoleri a mabanja a ana a Giliyadi mwana wa Makiri,+ mwana wa Manase, ochokera kumabanja a ana a Yosefe, anafika ndi kulankhula ndi Mose ndi akalonga omwe anali atsogoleri a ana a Isiraeli.
36 Atsogoleri a mabanja a ana a Giliyadi mwana wa Makiri,+ mwana wa Manase, ochokera kumabanja a ana a Yosefe, anafika ndi kulankhula ndi Mose ndi akalonga omwe anali atsogoleri a ana a Isiraeli.