-
Numeri 36:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ngati ana aakaziwa atakwatiwa ndi amuna a mafuko ena a Aisiraeli, ndiye kuti cholowa chawo chidzachotsedwa ku cholowa cha makolo athu, ndipo chidzawonjezedwa ku cholowa cha fuko limene aliyense adzakwatiweko. Zikadzatero ndiye kuti cholowa chathu cha malo chidzachepa.
-