Numeri 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho, mwana wamkazi aliyense amene walandira nawo cholowa pakati pa mafuko a Aisiraeli, azikwatiwa ndi mwamuna wa mʼbanja la fuko la makolo ake,+ kuti aliyense wa Aisiraeli azisunga cholowa chochokera kwa makolo ake.
8 Choncho, mwana wamkazi aliyense amene walandira nawo cholowa pakati pa mafuko a Aisiraeli, azikwatiwa ndi mwamuna wa mʼbanja la fuko la makolo ake,+ kuti aliyense wa Aisiraeli azisunga cholowa chochokera kwa makolo ake.