Numeri 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho, mwana wamkazi aliyense amene walandira nawo cholowa pakati pa mafuko a ana a Isiraeli, azikwatiwa ndi mwamuna wa m’banja la fuko la bambo ake,+ kuti aliyense wa ana a Isiraeli azilandira cholowa chochokera kwa makolo ake.
8 Choncho, mwana wamkazi aliyense amene walandira nawo cholowa pakati pa mafuko a ana a Isiraeli, azikwatiwa ndi mwamuna wa m’banja la fuko la bambo ake,+ kuti aliyense wa ana a Isiraeli azilandira cholowa chochokera kwa makolo ake.