-
Yoswa 2:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Mayiyo anayankha kuti: “Zikhale momwemo.”
Atatero anawauza kuti azipita ndipo iwo ananyamuka. Kenako mayiyo anamanga chingwe chofiira chija pawindopo.
-