-
Yoswa 2:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Pamenepo mkaziyo anati: “Zikhale monga mwanenera.”
Atatero anawauza kuti azipita, ndipo iwo ananyamuka. Kenako mkaziyo anamanga chingwe chofiira chija pawindopo.
-