Yoswa 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo matumba achikopa a vinyowa anali atsopano pamene timathiramo vinyo, koma tsopano angʼambika.+ Onaninso zovala ndi nsapato zathuzi, zangʼambika chifukwa cha kutalika kwa ulendo.”
13 Ndipo matumba achikopa a vinyowa anali atsopano pamene timathiramo vinyo, koma tsopano angʼambika.+ Onaninso zovala ndi nsapato zathuzi, zangʼambika chifukwa cha kutalika kwa ulendo.”